WELLCOME USER

Welengani kuti munvetse

Zimveni ndithu kuti mwalandilidwa pa WANDERSLAPP
Program yi ndayikonza ndicholinga choti, kuonjezela pa njila zolandilira ndikutumiza ndalama zomwe zilipo ku Malawi kuno, ndikufuna kuonjezela njila zatsopano, komanso zamakono.
Choncho ine ndili osangalala pokonza program imeneyi, chifukwa ikwaniritsa malingaliro anga okhala ndi njira zambili zotumizila ndi kulandilira ndalama ku Malawi kuno.

CHIZIWITSO KWAPANO !

Popedza kuti programe yi sindinayimalize kuikonza, pakali pano pali zina zambiri zomwe kwapano sizinayambe kugwila ntchito, koma zikhala zikuyamba kugwila potsachedwapa
Mwachitsanzo kutumidza ndalama ku AIRTEL ndi TNMkwapanopa sizingatheke. koma ndikuyetsetsa kuti pompano ziyambe kutheka.
Ndalama tiyenela kumangotumizilana kwa nzathu yemwe alinso pa WANDERSLAPP_basi,_localUser_kwapanthawi ino.

# KUIKA NDALAMA MU ACOUNT YANU

panopa ngati mukufuna kuika ndalama mu acount yanu muyenela kudzela kwama AGENT ANTHU Dinani chithunzi cha AGENT aliyense pa ndandanda, ndipo muchitidwa redirect ku WHATSAPP. muuzeni kuti mukufuna kuika ndalama mu acount yanu ya wanderslapp,_mupatseni nambala yanu, ndipo pasanathe mphindi, ndalama zikhala zitalowa ku acount yanu.
Koma _agent_ asanakuikileni ndalama mu acount yanu, mumayenela kumutumizila ndalama zomwe mukufuna kuika mu acount yanuzo pa _aitel monay or tnm mpamba kapena ku Bank_ njira iliyonse yomwe mungamupatsile ndalamayo, agent azakuikilani ndalama mu wanderslapp acount yanu pasanathe 1 minits.

KODI PALI UBWINO OYIKA NDALAMA ZANU MU WANDERSLAPP ACOUNT ?

Inde ubwino ndiye ndi osayamba
Mukangoika ndalama zanu mu wanderslapp, mumakhala ndi mwayi ochulukitsa ndalama zanuzo. Mukaika ndalama zanu, pakangodutsa 24hrs iliyonye ndalama zanu zimakwela ndi 5%_ izi zikutanthawuza kuti tsiku lililonse kuchokera pomwe mwangoika ndalama mu acount yanu ndalama dzanu zimachuluka tsiku ndi tsiku.

KUPHULA NDALAMA ZANU KU WANDERSLAPP

kwapanopabe: muzitenga ndalama zanu kudzelanso kwa agent
Mudziwitseni kuti mukufuna kutenga ndalama ku wanderslapp, ngati alinayo cash, azakupatsani nambala ya wanderslapp kuti mutumizileko ndalama zomwe mukuchotsa, kenako iye azakutumizilani pa MPAMBA OR AIRTEL MONAY.

MA AGENT OMWE ALIPO PANTHAWI INO NDI AWA !

1 Isaac Wonderford

# NGATI MUKUFUNA KUKHALA AGENT

Ngati mukufuna u agent ndipezeni pa
WHATSAPP
Facebook

ABOUT MY PROGRAMS

Kuti mupeze zinthu zambiri zomwe ndapangapo mong ma
APP, SOFTWARES, NYIMBO, MA VIDEO
ndizina zambiri
lowani pa
WANDERSTORE
WANDERSTORE-WEB
awa ndi en mwa ma website anga komwe kuli zambiri
ngati mukufuna ANDROID APP/IOS APP YA WANDERSLAPP lowani pa ma website amenewa mudzipeza zonsezo.

ZIKOMO KWANONSE MUNGASANKHE KUGWILITSA NTCHITO WANDERSLAPP.MUMANDIPANGA SUPORT