β‘
MA PROGRAM AMBIRI AKUBWELA POSACHEDWA
Panopa ndikuyesetsa kuti ndipange ma program ambiri mu design yanga yanga, ndifuna Suport yanu basi, mungathe kundipeza pa whatsap, email= wonderfordisaac@gmail.com, Call= 0899535951, ndi njila izi mutha kundiuza zomwe mukufuna zizipezeka pa mudzi pano. Mulungu azikudalitsani nonse mumandipanga suporp.
Ngati mukufuna kuti app/nyimbo yanu tiyike pano ndilankhuleni,
NYIMBO MWK500
APP MWK1000
SUPORT ME Please
ndimakunyadilani nonse