Nsungwana mukumuona pachithunziwu ndi nchemali wanga.
sister wangayu analemba nawo mayeso a STD 8, ndipo amusankhila ku,
Mulanje Boading Secondery School.
Ku school ku fees ndi 205,000. Ndalamayi kunena zoona kwaine potengela
mmene ndimapezera ndiyayikulu kwambili, makolonso nawo amadalira ine kuti
ndiwaponyele ya nchele.
Ndiye ndabweletsa nkhaniyi pano kuti mwina ngati nkotheka ena a mtima wa chifundo,
atithandizeko mwakufuna ndi kukoma mtima kwawo, osati mokakamizika ayi. Chonde abale
anga inu okondedwa, chonde ndikukupemphani🙏. Chimveni muntima.
Ndipo dziwani kuti ndizathokoza kwambiri ngati mutachitapo kanthu, ndipo ndizayamikila
chilichonse chomwe mungachite kwa ine, mwakufuna kwanu.
Dziwani izi:
Mungathe kulandila Madalitso chifukwa cha K100 yomwe mungapeleke
ndimtima wanu onse
ndikufunilani zabwino zonse.
pitilizani kusangalala ndi website ino.
pa website yi pali zambili
monga;
Kuphunzila kupanga website step by step
ma video, nyimbo, nsika, kucheza, nyimbo ndi dzina zambiri